Chichewa - The Importance of Child Discipline and Honoring Your Parents

Page 1


KufunikaKolangiza AnandiKulemekeza MakoloAnu

Phunzitsamwanam’njirayake; ndipoangakhaleatakalamba sadzachokamo.

Miyambo22:6

Pakutimakolo

Taonani,anandiwocholandirachaYehova:ndipochipatsocham'mimbandichomphotho yake.Salmo127:3

Wopandandodoadanandimwanawake;komawomkondaamlangamsanga.

Miyambo13:24

PakuopaYehovamulichikhulupirirocholimba,ndipoanaakeadzakhalandipothawirapo.

Miyambo14:26

Langamwanawakopamenechiyembekezochilipo,moyowakousalekekulirakwake.

Miyambo19:18

Utsiruumangidwamumtimamwamwana;komandodoyachilangoidzauingitsirakutali.

Miyambo22:15

Usam’manechilangomwana;Ukamukwapulandindodo,ndipoudzapulumutsamoyowake kugehena.Miyambo23:13-14

Ndodondichidzudzulozipatsanzeru;Miyambo29:15

Langamwanawako,ndipoadzakupumitsa;indeadzakondweretsamoyowako.

Miyambo29:17

NdipoanaakoonseadzaphunzitsidwandiYehova;ndipomtenderewaanaakoudzakhala

waukulu.Yesaya54:13

Iyeameneakondamwanawaceamgwiraiyekaŵirikaŵirindodo,kutiiye akasangalalendiiyepamapetopake.Wolangamwanawaceadzakondweranaye, Nadzakondweranayemwaamnzace.Wophunzitsamwanawaceacititsamdani cisoni;Ngakhaleatatewaceafa,alingatisanafa,pakutiwasiyawinawongaiyemwini.

Pameneiyeanalindimoyo,iyeanaonandipoanakondweramwaiye:ndipopamene iyeanafaiyesanamvechisoni.Anasiyam’mbuyomwakewobwezerachilangoadani ake,ameneadzabwezerachifundokwaanzake.Wosezamwanawaceadzamanga mikwingwirimayace;ndipomatumboakeadzanjenjemerandikulirakulikonse.

Kavalowosathyokasakhalawamutu;Petamwanawako,ndipoadzakuchititsa mantha:Seweraninaye,ndipoadzakuvutitsani.Usasekenaye,kutiungakhalendi cisoninaye,kapenakukukutamanopamapetopake.Musamupatseufulupaubwana wake,ndipomusayang'anirepakupusakwake.Uweramitsekhosilakealiwamng’ono, ndikum’menyam’nthitipamenealimwana,kutiangaumire,ndikusamveraiwe,ndi kubweretsachisonimumtimamwako.Langamwanawako,ndikumgwirantchito, kutichiwerewerechakechingakuchimwitse.Sirach30:1-13

Pakutiana

Lemekezaatatewakondiamako,kutimasikuakoachulukem'dzikolimeneYehova

Mulunguwakoakupatsaiwe.EKSODO20:12

Mwanawanga,usapeputsekulangakwaYehova;musatopendikulangakwace: PakutiameneYehovaamkondaamlanga;mongaatatemwanaameneakondwera naye.Miyambo3:11-12

MiyamboyaSolomo.Mwanawanzeruakondweretsaatate;Komamwanawopusa akhumudwitsaamake.Miyambo10:1

Mveraatatewakoameneanakubala,ndipousapeputseamakoatakalamba.

Miyambo23:22

Ananu,mveraniakukubalanimwaAmbuye,pakutiichin’chabwino.Lemekezaatate wakondiamako;(ndilondilolamuloloyambalokhalanalolonjezano)kutikukhale bwinondiiwe,ndikutiukhalewanthawipadzikolapansi.Aefeso6:1-3

Lemekezaatatewakondimtimawakowonse,ndipousaiwalezowawazaamako.

Kumbukiranikutimunabadwamwaiwo;ndipomungawabwezerebwanjizimene adakuchitirani?Sirach7:27-28

Anainu,ndimvereniineatatewanu,ndikuchitapambuyopake,kutimukhaleotetezeka.

PakutiYehovawapatsaatateulemupaana,nakhazikaulamulirowaamakepaana.

Wolemekezaatatewaceacitacotetezerakwamacimoace;Wolemekezaatatewace adzakondwerandianaace;ndipopameneapemphera,adzamveka.Wolemekezaatatewace adzakhalandimoyowautali;ndipowomveraYehovaadzakhalachitonthozokwaamake.

WoopaYehovaadzalemekezaatatewace,nadzatumikiraatatewace,mongaambuyeace.

Lemekezaatatewakondiamako,m’mawundim’ntchito,kutidalitsolochokerakwaiwo likadzekwaiwe.Pakutidalitsolaatatelikhazikitsanyumbazaana;komatembererolaamake lizulamaziko.Usadzitamandirendimanyaziaatatewako;pakutimanyaziaatatewakoalibe ulemererokwaiwe.Pakutiulemererowamunthuuchokerakuulemuwaatatewake;ndi mayiwamanyazindichitonzokwaana.Mwanawanga,thandizaatatewakomuukalamba wawo,ndipousawamvetsechisonimasikuonseamoyowawo.Ndipongatikuzindikira kwakekwalephera,mupirirenaye;ndipousamnyozepameneulimumphamvuzakozonse. Pakuticipulumutsocaatatewakosidzaiwalika;ndipom'malomwazoipazidzawonjezedwa kukumangaiwe.Patsikulakusaukakwakochidzakumbukiridwa;machimoakonso adzasungunuka,mongamadzioundanam’nyengoyofunda.Wosiyaatatewakealingati wonyoza;ndipoiyewokwiyitsaamakewotembereredwa:ndiMulungu.Sirach3:1-16

Ngatitidzalangaanaathu,adzaliratsopanokomaadzasangalalam’tsogolo.

Ngatisitilangaanaathu,adzasangalalapanopakomaadzaliram’tsogolo.

Ananditsogololadzikolathu.Komaakadzakalambaopandamwambo,tsogolola dzikolathulidzakhalalotani?

Zizolowezizonsezoipazamunthuwamkulundizijazomwesizinawongoleredwe kapenakulangidwaalimwana.Tiyenerakuleraanaameneamaopa,kukonda,ndi kumveraMulungu.

Ndinatengadongolamoyo

Ndikuliumbamofatsatsikunditsiku

Ndinabweransozakazitapita

Analimunthuyemwendimamuyang'ana

Iyeamavalabezowonekabwino

ndiposindingathekumusinthanso.

Turn static files into dynamic content formats.

Create a flipbook
Issuu converts static files into: digital portfolios, online yearbooks, online catalogs, digital photo albums and more. Sign up and create your flipbook.