Hagai
MUTU1
1ChakachachiŵirichamfumuDariyo,mweziwachisanundi chimodzi,tsikuloyambalamwezi,mauaYehovaanadza mwaHagaimnenerikwaZerubabelemwanawaSealatiyeli, kazembewaYuda,ndikwaYoswamwanawamfumu Yehosadaki,mkuluwaansembe,kuti, 2Yehovawamakamuatero,Anthuawaakunenakuti, ‘Nthawisiinafike,nthawiyomanganyumbayaYehova
3PamenepomauaYehovaanadzamwaHagaimneneri,kuti, 4Kodindinthawiyanu,inu,yokhalam’nyumbazanu zomangika,ndinyumbaiyiyapasuka?
5CifukwacaceateroYehovawamakamu;Lingaliraninjira zanu
6Mwafesazambiri,komamudabweretsapang’ono;mudya, komasimukhuta;mumwa,komasimukhutandichakumwa; mubvala,komapalibewofunda;ndiiyewolandiramalipiro alandirakutiayiikem’thumbalobowoka
7AteroYehovawamakamu;Lingaliraninjirazanu
8Kweranikuphiri,tengamitengo,nimumangenyumbayo; ndipondidzakondweranalo,ndipondidzalemekezedwa,’ wateroYehova
9Munayembekezerazambiri,komatawonani,zidakhala zazing’ono;ndipom’menemunabweranayokunyumba ndinauombaChifukwachiyani?wateroYehovawamakamu Chifukwachanyumbayangayapasuka,ndipoinu akuthamangirayensekunyumbayake.
10Chifukwachakethambolalekandimamechifukwachainu, ndidzikolapansilalekekazipatsozake
11Ndipondinaitanachilalapadziko,ndipamapiri,ndi patirigu,ndipavinyo,ndipamafuta,ndipadzikolapansi,ndi paanthu,ndipang’ombe,ndipazowetapantchitozonseza manja.
12PamenepoZerubabelemwanawaSealatieli,ndiYoswa mwanawaYehosadaki,mkuluwaansembe,ndiotsalaonsea anthu,anamveramauaYehovaMulunguwao,ndimaua Hagaimneneri,mongaYehovaMulunguwaoanawauza ndipoanthuanaopapamasopaYehova
13PamenepoHagai,mthengawaYehovam’uthengawa Yehova,ananenandianthu,kuti,Inendilindiinu,atiYehova 14NdipoYehovaanautsamzimuwaZerubabelemwanawa Sealatiyeli,bwanamkubwawaYuda,ndimzimuwaYoswa mwanawaYehosadaki,mkuluwaansembe,ndimzimuwa otsalaonseaanthu;ndipoanadzanagwiranchitom’nyumba yaYehovawamakamu,Mulunguwao; 15Tsikula24lamweziwachisanundichimodzi,m’chaka chachiwirichamfumuDariyo
MUTU2
1Mweziwacisanundiciwiri,tsikulamakumiawirindi limodzilamweziwo,mauaYehovaanadzamwamneneri Hagai,kuti,
2LankhulatsonokwaZerubabelemwanawaSealatiyeli, kazembewaYuda,ndiYoswamwanawaYehosadaki,mkulu waansembe,ndiotsalaaanthu,kuti,
3Ndaniwatsalamwainuameneadawonanyumbaiyimu ulemererowakewoyamba?ndipomucipenyabwanjitsopano? Kodisichirim’masomwanungatichabe?
4Komatsopanolimbika,iweZerubabele,atiYehova;ndipo limbikaiweYoswamwanawaYehosadaki,mkuluwa
ansembe;ndipokhalaniamphamvu,inunonseanthua m’dziko,atiYehova,ndipogwiranintchito; 5Mongamwamauamenendinapanganananu,muja munaturukam’Aigupto,mzimuwangaukhalabepakatipanu; 6PakutiateroYehovawamakamu;Komakamodzi,katsala kanthawi,ndipondidzagwedezamiyamba,ndidzikolapansi, ndinyanja,ndimtunda; 7Ndidzagwedezaamitunduonse,+ndipochokhumbacha amitunduonsechidzafika,+ndipondidzadzazanyumbaiyi ndiulemerero,”+wateroYehovawamakamu 8Silivandiwanga,golidendiwanga,atiYehovawamakamu 9Ulemererowotsirizawanyumbaiyiudzakhalawaukulu kuposawoyamba,atiYehovawamakamu,ndipom’maloano ndidzapatsamtendere,’+wateroYehovawamakamu
10Tsikulamakumiawirimphambuanayilamwezi wachisanundichinayi,m’chakachachiwirichaDariyo,+ mawuaYehovaanafikakudzeramwamneneriHagai,+kuti: 11AteroYehovawamakamu;Funsatsopanoansembeza chilamulo,ndikuti, 12Munthuakanyamulanyamayopatulikam’mphepetemwa chovalachake,nakhudzamkanjowakemkate,kapena mphodza,kapenavinyo,kapenamafuta,kapenachakudya chirichonse,kodichidzakhalachopatulika?Ndipoansembe anayankhanati,Iyayi.
13PamenepoHagaianati,Munthuwodetsedwachifukwacha mtemboakakhudzachilichonsemwaizi,kodichidzakhala chodetsedwa?Ndipoansembeanayankhanati,Chidzakhala chodetsedwa
14PamenepoHagaianayankha,nati,Momwemoanthuawa, ndimtunduuwuulipamasopanga,atiYehova;ndi momwemonsontchitoiliyonseyamanjaawo;ndipochimene aperekapameneponchodetsedwa
15Tsopano,inendikukupemphaniinu,lingaliranikuyambira lerokupitam’tsogolo,kuyambirapamenemwalausanaikidwe pamwalawinam’kachisiwaYehova;
16Kuyambiramasikuomwewo,munthuakafikapamuluwa miyesomakumiawiri,panalikhumikoma;
17Ndinakukanthanindichimphepo,ndichinoni,ndimatalala, pantchitozonsezamanjaanu;komasimunatembenukirakwa Ine,atiYehova
18Lingaliranitsopanokuyambiralerokupitam’tsogolo, kuyambiratsikulamakumiawirimphambuanailamwezi wachisanundichinayi,kuyambiratsikulijaanamangamaziko akachisiwaYehova,lingaliranizimenezo.
19Kodimbeuzikadalim’nkhokwe?inde,mpesa,ndimkuyu, ndimakangaza,ndimtengowaazitonasizinabale;kuyambira lerondidzakudalitsani.
20NdipomauaYehovaanadzansokwaHagaipatsikula24 lamwezi,kuti,
21NenakwaZerubabelekazembewaYuda,kuti, Ndidzagwedezakumwambandidzikolapansi;
22Ndidzagubuduzamipandoyamaufumu,ndipo ndidzawonongamphamvuzamaufumuaamitundu;ndipo ndidzagubuduzamagareta,ndiiwookweramo;ndiakavalo ndiokwerapoawoadzatsika,yensendilupangalambale wake.
23Tsikulimenelo,atiYehovawamakamu,ndidzakutenga iweZerubabele,mwanawaSealatiyeli,mtumikiwanga,ati Yehova,ndipondidzakusandutsangatichosindikizira;pakuti ndakusankhaiwe,atiYehovawamakamu